Nehemiya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho tinapitiriza kumanga mpandawo, ndipo khoma lonse linalumikizana mpaka kufika hafu ya kutalika kwake. Anthu anapitiriza kukhala ndi mtima wogwira ntchito.+
6 Choncho tinapitiriza kumanga mpandawo, ndipo khoma lonse linalumikizana mpaka kufika hafu ya kutalika kwake. Anthu anapitiriza kukhala ndi mtima wogwira ntchito.+