Ezara 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu mfumu dziwani kuti ife tinapita kuchigawo+ cha Yuda kunyumba ya Mulungu wamkulu.+ Kumeneko takapeza kuti nyumbayo akuimanga ndi miyala yochita kuigubuduzira pamalo ake ndiponso akuika matabwa m’makoma ake. Iwo akugwira ntchitoyo mwakhama ndipo ikupita patsogolo. Mlaliki 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nthawi yakupha+ ndi nthawi yochiritsa.+ Nthawi yogumula ndi nthawi yomanga.+ Akolose 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chilichonse chimene mukuchita, muzichichita ndi moyo wanu wonse+ ngati kuti mukuchitira Yehova,+ osati anthu,
8 Inu mfumu dziwani kuti ife tinapita kuchigawo+ cha Yuda kunyumba ya Mulungu wamkulu.+ Kumeneko takapeza kuti nyumbayo akuimanga ndi miyala yochita kuigubuduzira pamalo ake ndiponso akuika matabwa m’makoma ake. Iwo akugwira ntchitoyo mwakhama ndipo ikupita patsogolo.
23 Chilichonse chimene mukuchita, muzichichita ndi moyo wanu wonse+ ngati kuti mukuchitira Yehova,+ osati anthu,