Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 31:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Uwabwezere+ Amidiyani+ pa zimene anachitira ana a Isiraeli. Pambuyo pake udzaikidwa m’manda kuti ukagone ndi makolo ako.”+

  • Yeremiya 48:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Wotembereredwa ndi munthu wozengereza kugwira ntchito imene Yehova wamupatsa.+ Wotembereredwa ndi munthu wopewa kukhetsa magazi ndi lupanga lake.

  • Ezekieli 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mupheretu nkhalamba, anyamata, anamwali, tiana, ndi amayi.+ Koma musayandikire munthu aliyense amene ali ndi chizindikiro,+ ndipo muyambire pamalo anga opatulika.”+ Chotero iwo anayambira kupha akuluakulu amene anali panyumbapo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena