Salimo 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musalole kuti phazi la anthu odzikweza lindipondereze.+Ndipo musalole dzanja la anthu oipa kundipitikitsa kuti ndikhale wothawathawa.+ Mateyu 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Afarisi anachoka ndi kukapangana kuti am’kole m’mawu ake.+
11 Musalole kuti phazi la anthu odzikweza lindipondereze.+Ndipo musalole dzanja la anthu oipa kundipitikitsa kuti ndikhale wothawathawa.+