Ezara 2:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Ana a ansembe+ anali awa: ana a Habaya, ana a Hakozi,+ ana a Barizilai+ amene anatenga mkazi pakati pa ana aakazi a Barizilai+ Mgiliyadi n’kuyamba kutchedwa ndi dzina lawo.
61 Ana a ansembe+ anali awa: ana a Habaya, ana a Hakozi,+ ana a Barizilai+ amene anatenga mkazi pakati pa ana aakazi a Barizilai+ Mgiliyadi n’kuyamba kutchedwa ndi dzina lawo.