Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 17:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, Davide atangofika ku Mahanaimu, Sobi mwana wamwamuna wa Nahasi, wochokera ku Raba,+ mzinda wa ana a Amoni,+ komanso Makiri+ mwana wa Amiyeli,+ wochokera ku Lo-debara ndi Barizilai+ Mgiliyadi wochokera ku Rogelimu,+

  • 2 Samueli 19:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiyeno Barizilai+ Mgiliyadi nayenso anatsika kuchokera ku Rogelimu. Iye anapita ku Yorodano pamodzi ndi mfumu. Barizilai anaperekeza mfumu mpaka kukafika ku Yorodano.

  • 1 Mafumu 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Ana a Barizilai+ Mgiliyadi uwasonyeze kukoma mtima kosatha. Azikhala pakati pa anthu odyera nawe limodzi patebulo,+ chifukwa anandithandiza+ pa nthawi imene ndinali kuthawa m’bale wako Abisalomu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena