Ezara 2:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Ndiyeno ansembe, Alevi, anthu ena,+ oimba, alonda a pazipata, Anetini ndi Aisiraeli onse anayamba kukhala m’mizinda yawo.+
70 Ndiyeno ansembe, Alevi, anthu ena,+ oimba, alonda a pazipata, Anetini ndi Aisiraeli onse anayamba kukhala m’mizinda yawo.+