Deuteronomo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ukamanga nyumba yatsopano uzimanganso kampanda padenga*+ la nyumbayo kuopera kuti ungaike mlandu wa magazi panyumba yako ngati munthu atagwa kuchokera padengapo. Machitidwe 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsiku lotsatira, ulendo wawo uli mkati komanso akuyandikira mzindawo, Petulo anakwera padenga*+ kukapemphera cha m’ma 12 koloko masana.*+
8 “Ukamanga nyumba yatsopano uzimanganso kampanda padenga*+ la nyumbayo kuopera kuti ungaike mlandu wa magazi panyumba yako ngati munthu atagwa kuchokera padengapo.
9 Tsiku lotsatira, ulendo wawo uli mkati komanso akuyandikira mzindawo, Petulo anakwera padenga*+ kukapemphera cha m’ma 12 koloko masana.*+