Yoswa 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mose mtumiki wa Yehova atamwalira, Yehova analankhula ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, mtumiki+ wa Mose, kuti: Aheberi 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti ngati Yoswa+ anawalowetsa m’malo ampumulo,+ Mulungu sakananenanso pambuyo pake+ za tsiku lina.
1 Mose mtumiki wa Yehova atamwalira, Yehova analankhula ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, mtumiki+ wa Mose, kuti:
8 Pakuti ngati Yoswa+ anawalowetsa m’malo ampumulo,+ Mulungu sakananenanso pambuyo pake+ za tsiku lina.