Ekisodo 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti chofunda chake n’chomwecho.+ Imeneyo ndi nsalu yake yakunja. Adzafunda chiyani pogona? Ndiyeno akandilirira, ine ndidzamumvera ndithu, chifukwa ndine wachifundo.+ Salimo 103:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wachifundo ndi wachisomo,+Wosakwiya msanga ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+
27 Pakuti chofunda chake n’chomwecho.+ Imeneyo ndi nsalu yake yakunja. Adzafunda chiyani pogona? Ndiyeno akandilirira, ine ndidzamumvera ndithu, chifukwa ndine wachifundo.+