1 Mafumu 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzakhaladi pakati pa ana a Isiraeli,+ ndipo sindidzasiya anthu anga, Aisiraeli.”+ Salimo 106:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+
45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+