Numeri 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Yehova anati: “Chabwino, ndakhululuka chifukwa cha mawu ako.+ 1 Samueli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya+ anthu ake, pakuti Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+
22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya+ anthu ake, pakuti Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+