Ezara 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Akuluakuluwo anatiyankha kuti: ‘Ife ndife atumiki a Mulungu wakumwamba ndi dziko lapansi,+ ndipo tikumanganso nyumba imene inamangidwa zaka zambiri zapitazo, imene mfumu yaikulu ya Isiraeli inamanga ndi kuimaliza.+
11 “Akuluakuluwo anatiyankha kuti: ‘Ife ndife atumiki a Mulungu wakumwamba ndi dziko lapansi,+ ndipo tikumanganso nyumba imene inamangidwa zaka zambiri zapitazo, imene mfumu yaikulu ya Isiraeli inamanga ndi kuimaliza.+