Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 124:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Thandizo lathu lili m’dzina la Yehova,+

      Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi.”+

  • Yesaya 45:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pakuti Yehova, Mlengi wa kumwamba,+ Mulungu woona,+ amene anaumba dziko lapansi ndi kulipanga,+ amene analikhazikitsa mwamphamvu,+ amene sanalilenge popanda cholinga, amene analiumba kuti anthu akhalemo,+ wanena kuti: “Ine ndine Yehova ndipo palibenso wina.+

  • Yona 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iye anayankha kuti: “Ndine Mheberi,+ ndipo ndimaopa+ Yehova Mulungu wakumwamba,+ amene anapanga nyanja ndi mtunda.”+

  • Chivumbulutso 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena