Genesis 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anadalitsa Abulamu kuti: “Mulungu Wam’mwambamwamba adalitse Abulamu,+Iye amene anapanga kumwamba ndi dziko lapansi.+ Salimo 102:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munaika kalekale maziko a dziko lapansi,+Ndipo kumwamba ndiko ntchito ya manja anu.+ Chivumbulutso 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye analumbira pa Iye wokhala+ ndi moyo kwamuyaya,+ amene analenga kumwamba ndi zokhala kumeneko, ndi dziko lapansi+ ndi zinthu za mmenemo,+ ndi nyanja ndi zinthu za mmenemo. Analumbira kuti: “Sipakhalanso kuchedwa ayi.+
19 Kenako anadalitsa Abulamu kuti: “Mulungu Wam’mwambamwamba adalitse Abulamu,+Iye amene anapanga kumwamba ndi dziko lapansi.+ Salimo 102:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munaika kalekale maziko a dziko lapansi,+Ndipo kumwamba ndiko ntchito ya manja anu.+ Chivumbulutso 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye analumbira pa Iye wokhala+ ndi moyo kwamuyaya,+ amene analenga kumwamba ndi zokhala kumeneko, ndi dziko lapansi+ ndi zinthu za mmenemo,+ ndi nyanja ndi zinthu za mmenemo. Analumbira kuti: “Sipakhalanso kuchedwa ayi.+
6 Iye analumbira pa Iye wokhala+ ndi moyo kwamuyaya,+ amene analenga kumwamba ndi zokhala kumeneko, ndi dziko lapansi+ ndi zinthu za mmenemo,+ ndi nyanja ndi zinthu za mmenemo. Analumbira kuti: “Sipakhalanso kuchedwa ayi.+