1 Mafumu 8:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Atero n’cholinga choti anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi adziwe+ kuti Yehova ndi Mulungu woona.+ Palibenso wina.+ Yesaya 46:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kumbukirani zinthu zoyambirira zimene zinachitika kalekale,+ kuti ine ndine Mulungu+ ndipo palibenso Mulungu wina,+ kapena aliyense wofanana ndi ine.+
60 Atero n’cholinga choti anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi adziwe+ kuti Yehova ndi Mulungu woona.+ Palibenso wina.+
9 Kumbukirani zinthu zoyambirira zimene zinachitika kalekale,+ kuti ine ndine Mulungu+ ndipo palibenso Mulungu wina,+ kapena aliyense wofanana ndi ine.+