Oweruza 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Yehova anawagulitsa+ kwa Yabini mfumu yachikanani, imene inali kulamulira ku Hazori.+ Mkulu wa gulu lake lankhondo anali Sisera,+ yemwe anali kukhala ku Haroseti-ha-goimu.+ Oweruza 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ana a Isiraeli anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Motero Yehova anawapereka m’manja mwa Amidiyani+ kwa zaka 7.
2 Choncho Yehova anawagulitsa+ kwa Yabini mfumu yachikanani, imene inali kulamulira ku Hazori.+ Mkulu wa gulu lake lankhondo anali Sisera,+ yemwe anali kukhala ku Haroseti-ha-goimu.+
6 Kenako ana a Isiraeli anayamba kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Motero Yehova anawapereka m’manja mwa Amidiyani+ kwa zaka 7.