Levitiko 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo zotsala za nsembe yambewu ndi za Aroni ndi ana ake, popeza ndi zopatulika koposa zochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.+ Levitiko 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Munthu akadya mosadziwa chinthu chopatulika,+ azibwezera chinthucho ndi kuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo ake asanu.+ Azipereka chinthu chopatulikacho kwa wansembe.
10 Ndipo zotsala za nsembe yambewu ndi za Aroni ndi ana ake, popeza ndi zopatulika koposa zochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.+
14 “‘Munthu akadya mosadziwa chinthu chopatulika,+ azibwezera chinthucho ndi kuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo ake asanu.+ Azipereka chinthu chopatulikacho kwa wansembe.