26 Iye azingothandizira abale ake m’chihema chokumanako pochita utumiki wawo, koma asatumikire. Umu ndi mmene uzichitira ndi Alevi malinga ndi ntchito zawo.”+
5 Pakuti iye ndi amene Yehova Mulungu wako wam’sankha pakati pa mafuko anu onse, kuti iye pamodzi ndi ana ake aimirire ndi kutumikira m’dzina la Yehova nthawi zonse.+