Nehemiya 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno ndinazindikira kuti magawo+ a Alevi sanali kuperekedwa kwa iwo, moti aliyense wa Aleviwo ndi oimba amene anali kutumikira anathawa ndipo anapita kumunda wake.+ Nehemiya 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zitatero ndinayamba kuimba mlandu+ atsogoleriwo+ ndi kuwafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani nyumba ya Mulungu woona yasiyidwa chonchi?”+ Pamenepo ndinawasonkhanitsa pamodzi ndipo ndinawaika pamalo awo ogwirira ntchito.
10 Ndiyeno ndinazindikira kuti magawo+ a Alevi sanali kuperekedwa kwa iwo, moti aliyense wa Aleviwo ndi oimba amene anali kutumikira anathawa ndipo anapita kumunda wake.+
11 Zitatero ndinayamba kuimba mlandu+ atsogoleriwo+ ndi kuwafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani nyumba ya Mulungu woona yasiyidwa chonchi?”+ Pamenepo ndinawasonkhanitsa pamodzi ndipo ndinawaika pamalo awo ogwirira ntchito.