Esitere 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Mfumukazi Esitere inayankha kuti: “Ngati mungandikomere mtima mfumu, ndipo ngati zingakukomereni, ndikupempha kuti mupulumutse moyo wanga+ komanso kuti musawononge anthu a mtundu wanga.+
3 Pamenepo Mfumukazi Esitere inayankha kuti: “Ngati mungandikomere mtima mfumu, ndipo ngati zingakukomereni, ndikupempha kuti mupulumutse moyo wanga+ komanso kuti musawononge anthu a mtundu wanga.+