Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Moredekai ndi amene analera+ Hadasa, amene ndi Esitere, mwana wa m’bale wa bambo ake,+ chifukwa analibe bambo kapena mayi. Mtsikanayu anali wooneka bwino ndi wokongola kwambiri.+ Bambo ndi mayi a mtsikanayu atamwalira, Moredekai anam’tenga ngati mwana wake.

  • Esitere 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno anapatsa Hataki kalata+ imene munali lamulo lochokera ku Susani+ lakuti Ayuda afafanizidwe. Anamupatsa kalata imeneyi kuti akaonetse Esitere ndi kumuuza+ kuti akaonekere kwa mfumu ndi kuipempha kuti iwakomere mtima,+ ndiponso kuti Esitere akachonderere mfumu mwachindunji m’malo mwa anthu a mtundu wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena