Esitere 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Esitere sanali kunena za abale ake ndi anthu a mtundu wake,+ monga mmene Moredekai+ anamulamulira.+ Esitere anali kuchita zimene Moredekai wanena monga mmene anali kuchitira pa nthawi imene Moredekai anali kumusunga.+
20 Esitere sanali kunena za abale ake ndi anthu a mtundu wake,+ monga mmene Moredekai+ anamulamulira.+ Esitere anali kuchita zimene Moredekai wanena monga mmene anali kuchitira pa nthawi imene Moredekai anali kumusunga.+