Esitere 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Esitere sananene za mtundu wa anthu ake+ kapena za abale ake, pakuti Moredekai anali atamulamula kuti asanene kalikonse.+ Mateyu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+
10 Esitere sananene za mtundu wa anthu ake+ kapena za abale ake, pakuti Moredekai anali atamulamula kuti asanene kalikonse.+
16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+