Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Moredekai ndi amene analera+ Hadasa, amene ndi Esitere, mwana wa m’bale wa bambo ake,+ chifukwa analibe bambo kapena mayi. Mtsikanayu anali wooneka bwino ndi wokongola kwambiri.+ Bambo ndi mayi a mtsikanayu atamwalira, Moredekai anam’tenga ngati mwana wake.

  • Esitere 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Esitere sanali kunena za abale ake ndi anthu a mtundu wake,+ monga mmene Moredekai+ anamulamulira.+ Esitere anali kuchita zimene Moredekai wanena monga mmene anali kuchitira pa nthawi imene Moredekai anali kumusunga.+

  • Aefeso 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ananu, muzimvera makolo anu+ mwa+ Ambuye, pakuti kuchita zimenezi n’chilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena