Miyambo 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ukafooka pa tsiku la masautso,+ mphamvu zako zidzakhala zochepa. Miyambo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuopa anthu n’kumene kumatchera msampha,+ koma wokhulupirira Yehova adzatetezedwa.+ Yohane 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aliyense wokonda moyo wake akuuwononga, koma wodana ndi moyo wake+ m’dziko lino akuusungira moyo wosatha.+
25 Aliyense wokonda moyo wake akuuwononga, koma wodana ndi moyo wake+ m’dziko lino akuusungira moyo wosatha.+