Esitere 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’masiku amenewo, pamene Moredekai anali kukhala pansi kuchipata cha mfumu, Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri za panyumba ya mfumu, amenenso anali alonda a pakhomo, anakwiya ndipo anafuna kupha+ Mfumu Ahasiwero. Esitere 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno atumiki a mfumu amene anali kuchipatako anayamba kufunsa Moredekai kuti: “N’chifukwa chiyani ukunyalanyaza lamulo la mfumu?”+ Esitere 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi yomweyo mfumu inauza Hamani kuti: “Fulumira, tenga chovala ndi hatchi monga mmene wanenera, ndipo ukachitire zimenezi Moredekai, Myuda, amene ali kuchipata. Uonetsetse kuti zonse zimene wanenazi zakwaniritsidwa.”+
21 M’masiku amenewo, pamene Moredekai anali kukhala pansi kuchipata cha mfumu, Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri za panyumba ya mfumu, amenenso anali alonda a pakhomo, anakwiya ndipo anafuna kupha+ Mfumu Ahasiwero.
3 Ndiyeno atumiki a mfumu amene anali kuchipatako anayamba kufunsa Moredekai kuti: “N’chifukwa chiyani ukunyalanyaza lamulo la mfumu?”+
10 Nthawi yomweyo mfumu inauza Hamani kuti: “Fulumira, tenga chovala ndi hatchi monga mmene wanenera, ndipo ukachitire zimenezi Moredekai, Myuda, amene ali kuchipata. Uonetsetse kuti zonse zimene wanenazi zakwaniritsidwa.”+