Esitere 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Hamani anakwiya kwambiri+ chifukwa anaona kuti Moredekai sanali kumuweramira ndi kumugwadira.+ Mlaliki 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usamafulumire kukwiya mumtima mwako,+ pakuti anthu opusa ndi amene sachedwa kupsa mtima.+