Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 koma sanakondwere naye Kaini ndi nsembe yake+ m’pang’ono pomwe. Chotero Kaini anapsa mtima kwambiri+ ndipo nkhope yake inagwa.

  • Esitere 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamapeto pake, Hamani anatuluka tsiku limenelo ali wokondwa+ komanso akusangalala kwambiri mumtima mwake. Koma atangoona Moredekai pachipata cha mfumu+ komanso kuti sanaimirire+ ndi kunthunthumira chifukwa cha iye,+ nthawi yomweyo Hamani anamukwiyira kwambiri+ Moredekai.

  • Miyambo 14:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena