Yobu 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuti mfuu yachisangalalo ya anthu oipa sikhalitsa,+Ndiponso kuti kusangalala kwa wampatuko kumakhala kwa kanthawi? Luka 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Tsoka inu amene mukukhuta tsopano, chifukwa mudzamva njala.+ “Tsoka inu amene mukuseka tsopano, chifukwa mudzamva chisoni ndi kulira.+ Yakobo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Imvani chisoni ndipo lirani.+ Kuseka kwanu kusanduke kulira, ndipo chisangalalo chanu chisanduke chisoni.+
5 Kuti mfuu yachisangalalo ya anthu oipa sikhalitsa,+Ndiponso kuti kusangalala kwa wampatuko kumakhala kwa kanthawi?
25 “Tsoka inu amene mukukhuta tsopano, chifukwa mudzamva njala.+ “Tsoka inu amene mukuseka tsopano, chifukwa mudzamva chisoni ndi kulira.+
9 Imvani chisoni ndipo lirani.+ Kuseka kwanu kusanduke kulira, ndipo chisangalalo chanu chisanduke chisoni.+