Salimo 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngakhale gulu lankhondo litamanga msasa kuti lindiukire,+Mtima wanga sudzachita mantha.+Ngakhale nkhondo yolimbana ndi ine itayambika,+Pameneponso ndidzadalira Mulungu.+ Salimo 139:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu kwambiri,+Ndipo anthu okupandukirani ndimanyansidwa nawo.+ Salimo 139:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndimadana nawo kwambiri.+Kwa ine akhala adani enieni.+ Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+
3 Ngakhale gulu lankhondo litamanga msasa kuti lindiukire,+Mtima wanga sudzachita mantha.+Ngakhale nkhondo yolimbana ndi ine itayambika,+Pameneponso ndidzadalira Mulungu.+
21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu kwambiri,+Ndipo anthu okupandukirani ndimanyansidwa nawo.+
28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+