Salimo 101:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Sindidzaika maso anga pa chinthu chilichonse chopanda pake.+Ndimadana ndi zochita za opatuka pa choonadi.+Sindilola kuti zochita zawozo zindikhudze.+
3 Sindidzaika maso anga pa chinthu chilichonse chopanda pake.+Ndimadana ndi zochita za opatuka pa choonadi.+Sindilola kuti zochita zawozo zindikhudze.+