Esitere 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho atumiki onse a mfumu amene anali kuchipata cha mfumu+ anali kuwerama ndi kugwadira Hamani, pakuti mfumu inali italamula kuti anthu azim’chitira zimenezi. Koma Moredekai sanali kumuweramira kapena kumugwadira.+ Esitere 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako mfumu inati: “Kodi m’bwalo muli ndani?” Tsopano Hamani anali atalowa m’bwalo lakunja+ kwa nyumba ya mfumu kudzauza mfumu kuti apachike Moredekai pamtengo+ umene anamukonzera.
2 Choncho atumiki onse a mfumu amene anali kuchipata cha mfumu+ anali kuwerama ndi kugwadira Hamani, pakuti mfumu inali italamula kuti anthu azim’chitira zimenezi. Koma Moredekai sanali kumuweramira kapena kumugwadira.+
4 Kenako mfumu inati: “Kodi m’bwalo muli ndani?” Tsopano Hamani anali atalowa m’bwalo lakunja+ kwa nyumba ya mfumu kudzauza mfumu kuti apachike Moredekai pamtengo+ umene anamukonzera.