Esitere 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma ntchito zonse zamphamvu zimene anachita ndi mawu ofotokoza mphamvu zimene Moredekai+ anali nazo zimene mfumu inam’patsa,+ zinalembedwa m’Buku la zochitika+ za m’masiku a mafumu a Mediya ndi Perisiya.+
2 Koma ntchito zonse zamphamvu zimene anachita ndi mawu ofotokoza mphamvu zimene Moredekai+ anali nazo zimene mfumu inam’patsa,+ zinalembedwa m’Buku la zochitika+ za m’masiku a mafumu a Mediya ndi Perisiya.+