Esitere 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Hamani anaugwira mtima ndipo analowa m’nyumba yake. Kenako anatumiza uthenga kuti anzake ndi mkazi wake Zeresi+ abwere.
10 Koma Hamani anaugwira mtima ndipo analowa m’nyumba yake. Kenako anatumiza uthenga kuti anzake ndi mkazi wake Zeresi+ abwere.