-
Esitere 5:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Pamenepo mkazi wake Zeresi ndi anzake onsewo anamuuza kuti: “Mukonzetse mtengo+ wotalika mikono* 50. Ndiyeno m’mawa+ mukauze mfumu kuti apachike Moredekai pamtengowo.+ Mukatero mupite kuphwando ndi mfumu muli wosangalala.” Zimenezi zinaoneka zosangalatsa+ kwa Hamani, choncho anakonzetsa mtengowo.+
-
-
Esitere 6:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno Hamani anafotokozera Zeresi+ mkazi wake ndi anzake onse chilichonse chimene chinam’chitikira. Pamenepo amuna anzeru+ amene anali kum’tumikira ndi Zeresi mkazi wake anati: “Ngati n’zoona kuti Moredekai amene iwe wayamba kugonja pamaso pake ndi Myuda, sudzamugonjetsa koma udzagonja ndithu pamaso pake.”+
-