Deuteronomo 32:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+ Miyambo 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Woyenda mosalakwa adzapulumutsidwa,+ koma woyenda m’njira zokhota adzagwa mwadzidzidzi.+ Hoseya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+
35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+
9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+