Salimo 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mtima wanga wosagawanika ndiponso wowongoka unditeteze,+Pakuti chiyembekezo changa chili mwa inu.+ Salimo 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiweruzeni,+ inu Yehova, pakuti ine ndayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika,+Ndipo ndikudalira Yehova kuti ndisagwedezeke.+ Mateyu 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma amene adzapirire+ mpaka pa mapeto, ndiye amene adzapulumuke.+
21 Mtima wanga wosagawanika ndiponso wowongoka unditeteze,+Pakuti chiyembekezo changa chili mwa inu.+
26 Ndiweruzeni,+ inu Yehova, pakuti ine ndayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika,+Ndipo ndikudalira Yehova kuti ndisagwedezeke.+