1 Mbiri 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 A fuko la Isakara,+ amene anali ndi nzeru zotha kudziwa nthawi,+ ndi zimene Aisiraeli ayenera kuchita,+ analipo atsogoleri 200, ndipo iwo anali kulamulira abale awo onse. Mateyu 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma m’mawa mumanena kuti, ‘Lero kukuoneka kuti kugwa mvula, chifukwa kumwamba kwachita cheza koma kuli mdima wamvula.’ Mumadziwa kumasulira kaonekedwe ka kumwamba, koma simungathe kumasulira zizindikiro za nthawi ino.]]*+
32 A fuko la Isakara,+ amene anali ndi nzeru zotha kudziwa nthawi,+ ndi zimene Aisiraeli ayenera kuchita,+ analipo atsogoleri 200, ndipo iwo anali kulamulira abale awo onse.
3 Koma m’mawa mumanena kuti, ‘Lero kukuoneka kuti kugwa mvula, chifukwa kumwamba kwachita cheza koma kuli mdima wamvula.’ Mumadziwa kumasulira kaonekedwe ka kumwamba, koma simungathe kumasulira zizindikiro za nthawi ino.]]*+