Esitere 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno mfumu inalankhula ndi amuna anzeru,+ odziwa miyambo ya masiku amenewo.+ (Pakuti pa nkhani iliyonse, mfumu inali kufunsira kwa onse odziwa malamulo ndi nkhani zokhudzana ndi milandu. Luka 12:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Onyenga inu! Mumatha kuzindikira maonekedwe a dziko lapansi ndi kuthambo. Nanga zimakukanikani bwanji kuzindikira tanthauzo la zimene zikuchitika pa nthawi ino?+
13 Ndiyeno mfumu inalankhula ndi amuna anzeru,+ odziwa miyambo ya masiku amenewo.+ (Pakuti pa nkhani iliyonse, mfumu inali kufunsira kwa onse odziwa malamulo ndi nkhani zokhudzana ndi milandu.
56 Onyenga inu! Mumatha kuzindikira maonekedwe a dziko lapansi ndi kuthambo. Nanga zimakukanikani bwanji kuzindikira tanthauzo la zimene zikuchitika pa nthawi ino?+