Mateyu 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma m’mawa mumanena kuti, ‘Lero kukuoneka kuti kugwa mvula, chifukwa kumwamba kwachita cheza koma kuli mdima wamvula.’ Mumadziwa kumasulira kaonekedwe ka kumwamba, koma simungathe kumasulira zizindikiro za nthawi ino.]]*+ Luka 19:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Iye anati: “Iwe ukanazindikira+ lero zinthu zamtendere . . . koma tsopano zabisika kuti usathe kuziona.+
3 Koma m’mawa mumanena kuti, ‘Lero kukuoneka kuti kugwa mvula, chifukwa kumwamba kwachita cheza koma kuli mdima wamvula.’ Mumadziwa kumasulira kaonekedwe ka kumwamba, koma simungathe kumasulira zizindikiro za nthawi ino.]]*+
42 Iye anati: “Iwe ukanazindikira+ lero zinthu zamtendere . . . koma tsopano zabisika kuti usathe kuziona.+