Genesis 37:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Amidiyani aja anakagulitsa Yosefe ku Iguputo kwa Potifara. Potifara anali nduna ya panyumba ya Farao,+ ndiponso anali mkulu wa asilikali olondera mfumu.+ Esitere 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’masiku amenewo, pamene Moredekai anali kukhala pansi kuchipata cha mfumu, Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri za panyumba ya mfumu, amenenso anali alonda a pakhomo, anakwiya ndipo anafuna kupha+ Mfumu Ahasiwero.
36 Amidiyani aja anakagulitsa Yosefe ku Iguputo kwa Potifara. Potifara anali nduna ya panyumba ya Farao,+ ndiponso anali mkulu wa asilikali olondera mfumu.+
21 M’masiku amenewo, pamene Moredekai anali kukhala pansi kuchipata cha mfumu, Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri za panyumba ya mfumu, amenenso anali alonda a pakhomo, anakwiya ndipo anafuna kupha+ Mfumu Ahasiwero.