Ezara 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako tinapereka malamulo+ a mfumu kwa masatarapi*+ a mfumu ndi abwanamkubwa+ a kutsidya lina la Mtsinje.*+ Iwo anathandiza anthuwo+ ndiponso anathandiza panyumba ya Mulungu woona. Esitere 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Akalonga onse+ a m’zigawozo, masatarapi,*+ abwanamkubwa ndi onse ogwira ntchito+ za mfumu anali kuthandiza Ayudawo chifukwa anali kuopa+ Moredekai. Danieli 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Dariyo anaona kuti ndi bwino kuti aike masatarapi* 120 oyang’anira zigawo zonse za ufumu wake.+
36 Kenako tinapereka malamulo+ a mfumu kwa masatarapi*+ a mfumu ndi abwanamkubwa+ a kutsidya lina la Mtsinje.*+ Iwo anathandiza anthuwo+ ndiponso anathandiza panyumba ya Mulungu woona.
3 Akalonga onse+ a m’zigawozo, masatarapi,*+ abwanamkubwa ndi onse ogwira ntchito+ za mfumu anali kuthandiza Ayudawo chifukwa anali kuopa+ Moredekai.
6 Ndiyeno Dariyo anaona kuti ndi bwino kuti aike masatarapi* 120 oyang’anira zigawo zonse za ufumu wake.+