Salimo 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Oipa asolola lupanga ndipo akunga uta wawo,+Kuti agwetse osautsika ndi osauka,+Kuti aphe anthu amene njira zawo ndi zowongoka.+ Salimo 68:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Monga mmene mphepo imauluzira utsi, inunso muwauluze chimodzimodzi.+Ngati mmene phula limasungunukira chifukwa cha moto,+Anthu oipa awonongeke ndi kuchotsedwa pamaso pa Mulungu.+
14 Oipa asolola lupanga ndipo akunga uta wawo,+Kuti agwetse osautsika ndi osauka,+Kuti aphe anthu amene njira zawo ndi zowongoka.+
2 Monga mmene mphepo imauluzira utsi, inunso muwauluze chimodzimodzi.+Ngati mmene phula limasungunukira chifukwa cha moto,+Anthu oipa awonongeke ndi kuchotsedwa pamaso pa Mulungu.+