Yobu 36:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa mawu anga ndithu si onama.Wodziwa bwino zinthu kwambiri+ ali ndi inu. Salimo 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+ Salimo 104:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+Zonsezo munazipanga mwanzeru zanu.+Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.+
30 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+
24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+Zonsezo munazipanga mwanzeru zanu.+Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.+