1 Samueli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musalankhule modzikweza kwambiri anthu inu,Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,+Pakuti Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse.+Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.+ Yobu 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi mukudziwa mmene mtambo umaimira,+Ndiponso ntchito zodabwitsa za yemwe amadziwa zinthu bwino kwambiri?+
3 Musalankhule modzikweza kwambiri anthu inu,Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,+Pakuti Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse.+Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.+
16 Kodi mukudziwa mmene mtambo umaimira,+Ndiponso ntchito zodabwitsa za yemwe amadziwa zinthu bwino kwambiri?+