Yobu 42:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu munati, ‘Kodi amene akuphimba malangizo anga mopanda nzeruyu ndani?’+Chotero ine ndinalankhula, koma sindinali kuzindikiraZinthu zodabwitsa kwambiri kwa ine, zimene sindikuzidziwa.+ 1 Timoteyo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amenewa amafuna kukhala aphunzitsi+ a chilamulo+ koma sazindikira zimene akunena kapena mfundo zimene akuzilimbikira.
3 Inu munati, ‘Kodi amene akuphimba malangizo anga mopanda nzeruyu ndani?’+Chotero ine ndinalankhula, koma sindinali kuzindikiraZinthu zodabwitsa kwambiri kwa ine, zimene sindikuzidziwa.+
7 Amenewa amafuna kukhala aphunzitsi+ a chilamulo+ koma sazindikira zimene akunena kapena mfundo zimene akuzilimbikira.