Salimo 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova Mulungu wanga, mwatichitira zinthu zambiri zodabwitsa,+Ndipo mumatiganizira.+Palibe angafanane ndi inu.+Ndikafuna kulankhula ndi kunena za zodabwitsazo,Zimachuluka kwambiri moti sindingathe kuzifotokoza.+ Salimo 131:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 131 Inu Yehova, mtima wanga sunadzikweze,+Maso anga si onyada.+Sindinafune zinthu zapamwamba kwambiri,+Kapena zinthu zodabwitsa kwambiri.+ Salimo 139:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kwa ine ndi zovuta kwambiri kuti ndidziwe zinthu zonsezi.+Ndi zapamwamba kwambiri moti sindingathe kuzifikira.+
5 Inu Yehova Mulungu wanga, mwatichitira zinthu zambiri zodabwitsa,+Ndipo mumatiganizira.+Palibe angafanane ndi inu.+Ndikafuna kulankhula ndi kunena za zodabwitsazo,Zimachuluka kwambiri moti sindingathe kuzifotokoza.+
131 Inu Yehova, mtima wanga sunadzikweze,+Maso anga si onyada.+Sindinafune zinthu zapamwamba kwambiri,+Kapena zinthu zodabwitsa kwambiri.+
6 Kwa ine ndi zovuta kwambiri kuti ndidziwe zinthu zonsezi.+Ndi zapamwamba kwambiri moti sindingathe kuzifikira.+