Yobu 42:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu munati, ‘Kodi amene akuphimba malangizo anga mopanda nzeruyu ndani?’+Chotero ine ndinalankhula, koma sindinali kuzindikiraZinthu zodabwitsa kwambiri kwa ine, zimene sindikuzidziwa.+ Salimo 139:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kwa ine ndi zovuta kwambiri kuti ndidziwe zinthu zonsezi.+Ndi zapamwamba kwambiri moti sindingathe kuzifikira.+
3 Inu munati, ‘Kodi amene akuphimba malangizo anga mopanda nzeruyu ndani?’+Chotero ine ndinalankhula, koma sindinali kuzindikiraZinthu zodabwitsa kwambiri kwa ine, zimene sindikuzidziwa.+
6 Kwa ine ndi zovuta kwambiri kuti ndidziwe zinthu zonsezi.+Ndi zapamwamba kwambiri moti sindingathe kuzifikira.+