Yobu 42:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu munati, ‘Kodi amene akuphimba malangizo anga mopanda nzeruyu ndani?’+Chotero ine ndinalankhula, koma sindinali kuzindikiraZinthu zodabwitsa kwambiri kwa ine, zimene sindikuzidziwa.+ Salimo 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova Mulungu wanga, mwatichitira zinthu zambiri zodabwitsa,+Ndipo mumatiganizira.+Palibe angafanane ndi inu.+Ndikafuna kulankhula ndi kunena za zodabwitsazo,Zimachuluka kwambiri moti sindingathe kuzifotokoza.+ Salimo 131:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 131 Inu Yehova, mtima wanga sunadzikweze,+Maso anga si onyada.+Sindinafune zinthu zapamwamba kwambiri,+Kapena zinthu zodabwitsa kwambiri.+ Aroma 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?
3 Inu munati, ‘Kodi amene akuphimba malangizo anga mopanda nzeruyu ndani?’+Chotero ine ndinalankhula, koma sindinali kuzindikiraZinthu zodabwitsa kwambiri kwa ine, zimene sindikuzidziwa.+
5 Inu Yehova Mulungu wanga, mwatichitira zinthu zambiri zodabwitsa,+Ndipo mumatiganizira.+Palibe angafanane ndi inu.+Ndikafuna kulankhula ndi kunena za zodabwitsazo,Zimachuluka kwambiri moti sindingathe kuzifotokoza.+
131 Inu Yehova, mtima wanga sunadzikweze,+Maso anga si onyada.+Sindinafune zinthu zapamwamba kwambiri,+Kapena zinthu zodabwitsa kwambiri.+
33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?